Koma akuphika muma quotes umu😭😭😭😭😭😭 plz girl work hard palibe chinthu chosangalatsa ngat kutenga ndlama yako kukagulira chinthu without ma explanation kwa munthu winawake🙂👍 it's the best feeling
Mkutheka mamunayo mamufuna ndinu chabe.. Tweeting all this just because a fellow female is praying for a loving husband is a nasty behavior.. Get a life
Atsikana awiri ochita khalidwe loyendayenda ndilokonda kupakulisa kwa zidyamakanda mu nzinda wa Lilongwe, Riana Baggus ndi Patience Mwala, akutsadzulana ku WhatsApp kamba ka mchitidwe wachimasomaso. Oyamba akumveka ngati amakhala Kwa Mtsilizayo nde Riana.