Steven Chisale
@DJ_Maximum1
Followers
69
Following
23
Media
26
Statuses
66
An Entrepreneur, Pro. Dj at Maximum Entertainment, Producer and Presenter of Friday Night Jamz on PL FM. Works at Chidren of the Nations Malawi
Malawi
Joined June 2020
Pakati pa inuyo ndi bae amene amaponya zovala zakudza panja pa washing basket ndani?
0
0
0
Kodi bwanji ma video a ma ukwati akunja sitiona ma photographer onyamula chi ambullera chija? 🙆♂️🤷♂️ asking for myself
0
0
0
Ndimati ndipempheko, Zija zomaima pa umba wa maliro "nkumati anawa tisamala ife achibale" bwanji zitasiika?
0
0
1
Ma champagne poppers polani moto... zithuzi nzoti anthu amwe osati kuthila ma camera a anzanu..
0
0
1
Mmalo momuikiza mmapemphero mkazi chomuikira pa billboard ndi chani?
0
0
0
Mention your resident Pastor/Bishop/Prophet/Prophetes/overseer's name here or someone who impacted your life spiritually... let's show them some love..
0
0
0
Iwe ndalama ngati nchibisalilano chabwino wawina basi vumbuluka🤣
0
0
0
Guys you are now diluting the Amapiano genre and its fast losing salt. Leave the old school alone. You can't be doing remakes of all old time hits. Sizikukoma
0
0
0