AirtelMoneyMw Profile Banner
Airtel Money Malawi Profile
Airtel Money Malawi

@AirtelMoneyMw

Followers
1K
Following
2
Media
625
Statuses
774

Welcome to the official Twitter Handle of Airtel Money Malawi. Follow us for product updates, your queries and complaint resolution.

Joined April 2021
Don't wanna be here? Send us removal request.
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
2 days
Do you have a TNM number or that one friend does? Top Up Airtime to Neba’s line with your Airtel Money wallet! Zapa Izee​ ​Dial *211# and follow the steps below to enjoy recharges across networks, the first of it’s kind with Airtel Money. ​ #DigitalRecharge #MobiTopUpNeba
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
3 days
Phweketsani momwe mumagulira magetsi anu ndi Airtel Money!​ ​Gulani tokeni yanu ya magetsi mosavuta pogwiritsa ntchito MyAirtelApp kapena poyimba *211# ndi kuwalitsa m'nyumba mwanu lero!​ #AirtelMoney #BillPayment
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
3 days
𝗥𝘂𝗻𝗻𝗶𝗻𝗴 𝗹𝗼𝘄 𝗼𝗻 𝗮𝗶𝗿𝘁𝗶𝗺𝗲 𝗼𝗿 𝗯𝘂𝗻𝗱𝗹𝗲? Top up with Airtel Money, 𝗭𝗮𝗽𝗮 𝗜𝘇𝗲𝗲!​ ​Whether it’s catching up, calling home, or streaming your playlist. Use MyAirtelApp to stay connected. ​ #AirtelMoney #DigitalRecharge #MobiTop #ZapaIzee
0
0
1
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
4 days
Mongoyelekezera? Mwatumiza ndalama kangati chaka chino pa Airtel Money?​ ​Osanama😂​ ​#AirtelMoney
1
0
1
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
4 days
Muthandizeni Neba pamene mayunitsi amuvuta ndi Airtel Money​! Gwiritsani ntchito MyAirtelApp kapena imbani *211# ndi kutsatira ndondomeko zomwe zawonetsedwazo kuti mugulire mayunitsi oyimbira foni ku nambala ya neba.​ #AirtelMoney #DigitalRecharge #MobiTopUpNeba
0
0
1
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
8 days
Dziwani momwe kalipiridwe ka Thanzi Medical Cover kamayendera pa Airtel Money!​ ​*Tsatirani tsambali kuti muzidziwa zonse zokhudza Airtel Money❤️​ #AirteMoney #Thanzi #AirtelMoneyxWemas
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
8 days
𝗧𝗶𝘆𝗲𝗻𝗶 𝘁𝗶𝗸𝗮𝘀𝗮𝗻𝗴𝗮𝗹𝗮𝗹𝗲 𝗽𝗮 𝗰𝗵𝗶 𝗙𝗿𝗶𝗱𝗮𝘆!​🔥🔥 ​Gwiritsani ntchito Airtel Money kuti mulipire zokumwa ndi azinzake weekend imeneyi. Gwiritsani MyAirtelApp kapena imbani *211# polipira.​ #AirtelMoney #FridayMood
0
0
1
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
9 days
LIPIRANI FEES MOPANDA NKHAWA PA AIRTEL MONEY!​ ​Imbani *211#, sankhani 8 kenako 1 ndikulipira fees ku sukulu iliyonse yomwe ili ndi account ya 𝗖𝗲𝗻𝘁𝗲𝗻𝗮𝗿𝘆 𝗕𝗮𝗻𝗸 kuchokera ku wallet yanu ya Airtel Money. ​#CenteFees #AirtelMoneyxCentenaryBank #FeesPaymentMadeEasy
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
10 days
Kodi mumagwiritsa ntchito magetsi a Solar? ​ ​Lipirani modalirika pa Airtel Money ndi kuwalitsa m'nyumba mwanu. Gwiritsani ntchito MyAirtelApp kapena imbani *211# lero. ​ *Tsatirani tsambali kuti muzidziwa zonse zokhudza Airtel Money❤️​ #AirtelMoney #BillPayment
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
10 days
𝗞𝘂𝗰𝗵𝗲𝘇𝗮 𝗸𝗼𝗽𝗮𝗻𝗱𝗮 𝗺𝗮𝗹𝗶𝗿𝗲! ​ Gulani mayunitsi pa Airtel Money kuti muyankhulane ndi okondedwa anu kwa nthawi yayitali. Zapa Izee!​ *Tsatirani tsambali kuti muzidziwa zonse zokhudza Airtel Money❤️ #AirtelMoney #DigitalRecharge #ZapaIzee
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
11 days
Ndi chiticho apa chomwe chimakuphweketselani moyo pa Airtel Money?​ Muthanso kutchula chomwe apapa palibe. Tiuzeni m'musimu❤️👇🏽 #AirtelMoney
1
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
11 days
𝗣𝗮𝘆 𝘀𝗰𝗵𝗼𝗼𝗹 𝗳𝗲𝗲𝘀 𝗲𝗮𝘀𝗶𝗹𝘆 𝗮𝗻𝗱 𝗶𝗻𝘀𝘁𝗮𝗻𝘁𝗹𝘆 𝘄𝗶𝘁𝗵 𝗔𝗶𝗿𝘁𝗲𝗹 𝗠𝗼𝗻𝗲𝘆! ​Dial *211# and follow the simple steps shown to pay fees to any school with a Centenary Bank account with your Airtel Money wallet. ​ #CenteFees #AirtelMoneyxCentenaryBank
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
12 days
Sort out your water, electricity and TV subscription bills today with Airtel Money!​ ​ It's simple, instant and secure. Use MyAirtelApp or Dial *211# to enjoy convenience. ​ #AirtelMoney #MyAirtelApp #BillPayment
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
16 days
Recharge your airtime and bundles in seconds to stay connected - All with Airtel Money!​ ​Dial *211# or use MyAirtelApp - https://t.co/aw4VYdsBjj to top up your airtime and bundles instantly.​ #AirtelMoney #MobiTop #DigitalRecharge
0
0
1
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
19 days
BIZINESI ISAYIME CHIFUKWA CHA VALUE! Thamangitsanibe bizinesi ngakhale mulibe ndalama yokwanira M'godi tsopano ili pa 2 mukapita pa Menu yanu. Dziwani ngati mungathe kutenga kapena ngati muli pa Mgodi popita pa 7. Gwiritsani ntchito M'godi lero. Naye Agent ananale!
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
20 days
From the ground up, every dream takes work - and the right tools to build it. ​ ​Start strong this week with Airtel Money, your partner in every payment, plan, and progress. ​ #AirtelMoney #MondayMotivation #NewWeek
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
25 days
Education is the key to brighter futures. ​With Centefees on Airtel Money, paying school fees is now simpler, safer, and faster.​ ​Dial *211# and follow the simple steps shown to pay Centefees with your Airtel Money wallet.​ #AirtelMoneyxCentenaryBank #FeesPaymentMadeEasy
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
29 days
𝗟𝗜𝗣𝗜𝗥𝗔𝗡𝗜 𝗕𝗜𝗟𝗨 𝗬𝗔𝗡𝗨 𝗬𝗔 𝗠𝗔𝗗𝗭𝗜 𝗣𝗔 𝗔𝗜𝗥𝗧𝗘𝗟 𝗠𝗢𝗡𝗘𝗬!​ Gwiritsani ntchito MyAirtelApp kapena imbani *211# kuti mulipire ndi kukhala ndi madzi nthawi zonse. ​ #AirtelMoney #BillPayment #MyAirtelApp
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
30 days
𝗧𝗵𝗲 𝗲𝗮𝘀𝗶𝗲𝘀𝘁 𝗮𝗻𝗱 𝘀𝗺𝗮𝗿𝘁𝗲𝘀𝘁 𝘄𝗮𝘆 𝘁𝗼 𝗿𝗲𝗰𝗵𝗮𝗿𝗴𝗲 𝗮𝗻𝗱 𝘀𝘁𝗮𝘆 𝗰𝗼𝗻𝗻𝗲𝗰𝘁𝗲𝗱! 𝗭𝗮𝗽𝗮 𝗜𝘇𝗲𝗲!​ ​Top up airtime with your Airtel Money wallet today. Use MyAirtel App or Dial *211# to top up your airtime instantly.​ #DigitalRacharge #ZapaIzee
0
0
0
@AirtelMoneyMw
Airtel Money Malawi
1 month
𝗣𝗮𝘆 𝗳𝗲𝗲𝘀 𝘁𝗼 𝗮𝗻𝘆 𝘀𝗰𝗵𝗼𝗼𝗹 𝘄𝗶𝘁𝗵 𝗮 𝗖𝗲𝗻𝘁𝗲𝗻𝗮𝗿𝘆 𝗕𝗮𝗻𝗸 𝗮𝗰𝗰𝗼𝘂𝗻𝘁 𝘄𝗶𝘁𝗵 𝗔𝗶𝗿𝘁𝗲𝗹 𝗠𝗼𝗻𝗲𝘆! Dial *211# and follow the steps shown to pay Centefees with your Airtel Money wallet.​ #AirtelMoney #Centefees
0
0
1